Oryginalne teksty (piosenek)
cziczewa
Przekład
angielski
Mubwere
Oh, Sispence, oh oh oh
Ritaa.. Hello?
(Verse 1)
Munachoka kuti mukukasaka ndalama
Mpaka lero simunabwelerenso
Munachoka kutisiya ndi amai athu
Koma simunabwelere..
Simumatumizanso chithandizo kunyumba
Koma zoti mukuchita bwino tikumva
Sitimadziwa ngati mumatiganizira
Sitimadziwa ngati mumatikumbukira
(Chorus)
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba..
(Verse 2)
Tinakula, otilera anali mai athu
Kuvutika pamodzi ndi amai athu
Komanso mutangopita,
achimwene anatisiya
Ana anu akungolira,
Chilichonse kuvutikira
Phone yokha mukanatiimbira (hello?)
Kalata yokha mukanatilembera (you know)
Sitimadziwa ngati mumatiganizira
Sitimadziwa ngati mumatikumbukira
(Chorus)
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba
Mubwere kunyumba
Mubwelere kunyumba
(Bridge)
Ohh, mubwelere kunyumba
Oh, oh , oh ..
Mubwelere kunyumba
(Chorus)
Come
Oh, Sispence, oh oh oh
Ritaa... Hello?
(Verse 1)
You left, saying you’re going to look for money,
Till today
You never came back
You left us with our mother,
But you never came back.. you don’t even send any help back home,
But we’ve heard you’re doing so well
We don’t know if you think of us
We don’t know if you still remember us
(Chorus)
Come home
Come back home
Come home
Come back home..
(Verse 2)
We grew up, our mother raised us
Struggling together with our mother
And soon after you left, our brother died
Your children are just crying, struggling with everything
At least you could have phoned us (hello?)
At least you could have written us ( you know?)
We don’t know if you think of us, we don’t know if you still remember us
(Chorus)
Come home
Come back home
Come home
Come back home
( Bridge)
Ohh, come back home
Oh, oh oh..
Come back home
(Chorus)

Give a shoutout to Lucky01



Komentarze 1
Please, remove "Ritaa mubwere lyrics" from your translation.